2 Atesalonika 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Adzatero pa nthawi imene adzabwere kudzalandira ulemerero mogwirizana ndi oyera ake.+ Pa tsiku limenelo, onse amene anakhulupirira mwa iye, adzamusirira ndi kumuyang’anitsitsa, chifukwa pakati panu, munakhulupirira umboni umene tinapereka.
10 Adzatero pa nthawi imene adzabwere kudzalandira ulemerero mogwirizana ndi oyera ake.+ Pa tsiku limenelo, onse amene anakhulupirira mwa iye, adzamusirira ndi kumuyang’anitsitsa, chifukwa pakati panu, munakhulupirira umboni umene tinapereka.