1 Atesalonika 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti mukudziwa malamulo+ amene tinakupatsani mwa ulamuliro wa Ambuye Yesu. 1 Timoteyo 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Lamula achuma+ a m’nthawi* ino kuti asakhale odzikweza,+ ndiponso kuti asamadalire chuma chosadalirika,+ koma adalire Mulungu, amene amatipatsa mowolowa manja zinthu zonse kuti tisangalale.+ Tito 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndinakusiya ku Kerete+ kuti ukonze zinthu zosalongosoka ndi kuti uike+ akulu mumzinda uliwonse, malinga ndi malangizo+ amene ndinakupatsa.
17 Lamula achuma+ a m’nthawi* ino kuti asakhale odzikweza,+ ndiponso kuti asamadalire chuma chosadalirika,+ koma adalire Mulungu, amene amatipatsa mowolowa manja zinthu zonse kuti tisangalale.+
5 Ndinakusiya ku Kerete+ kuti ukonze zinthu zosalongosoka ndi kuti uike+ akulu mumzinda uliwonse, malinga ndi malangizo+ amene ndinakupatsa.