Tito 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amanena poyera kuti amadziwa Mulungu,+ koma amamukana ndi zochita zawo+ chifukwa ndi onyansa ndi osamvera, ndipo ndi osayenerera+ ntchito iliyonse yabwino.
16 Amanena poyera kuti amadziwa Mulungu,+ koma amamukana ndi zochita zawo+ chifukwa ndi onyansa ndi osamvera, ndipo ndi osayenerera+ ntchito iliyonse yabwino.