Afilipi 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma oyambawo akutero chifukwa cha mtima wokonda mikangano,+ osati ndi cholinga chabwino. Pakuti akungofuna kundiwonjezera masautso+ m’ndende muno. 2 Timoteyo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ndiponso ooneka ngati odzipereka kwa Mulungu+ koma amakana kuti mphamvu ya kudziperekako iwasinthe.+ Anthu amenewa uwapewe.+
17 Koma oyambawo akutero chifukwa cha mtima wokonda mikangano,+ osati ndi cholinga chabwino. Pakuti akungofuna kundiwonjezera masautso+ m’ndende muno.
5 ndiponso ooneka ngati odzipereka kwa Mulungu+ koma amakana kuti mphamvu ya kudziperekako iwasinthe.+ Anthu amenewa uwapewe.+