Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pamenepo Natani anauza Davide kuti: “Munthu ameneyo ndiwe! Choncho Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ine ndinakudzoza+ iwe kuti ukhale mfumu ya Isiraeli ndipo ndinakupulumutsa+ m’manja mwa Sauli.

  • Salimo 141:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza kukoma mtima kosatha,+

      Ndipo akandidzudzula ndiye kuti wandidzoza mafuta pamutu panga,+

      Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+

      Pakuti ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera.+

  • Miyambo 27:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Zilonda zovulazidwa ndi munthu wokukonda zimakhala zokhulupirika,+ koma kuti munthu wodana nawe akupsompsone pamafunika kumuchonderera.+

  • Agalatiya 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma Kefa+ atabwera ku Antiokeya,+ ndinamutsutsa pamasom’pamaso, chifukwa anali wolakwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena