Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 18:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiyeno Sauli anaponya mkondo uja+ ndi kunena kuti: “Ndilasa Davide ndi kumukhomerera kukhoma* ndi mkondowu!”+ Koma Davide anamuthawa, ndipo zimenezi zinachitika kawiri konse.+

  • 1 Samueli 19:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Zitatero, Sauli anafuna kulasa Davide kuti amukhomerere kukhoma ndi mkondo.+ Koma Davide anaulewa+ pamaso pa Sauli, moti mkondowo unalasa khoma. Pamenepo, Davide anathawa kuti adzipulumutse usiku umenewo.+

  • 1 Samueli 23:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tsopano Davide anayamba kukhala m’chipululu, m’malo ovuta kufikako. Iye anapitiriza kukhala m’dera lamapiri m’chipululu cha Zifi,+ ndipo Sauli anali kumufunafuna nthawi zonse,+ koma Mulungu sanam’pereke m’manja mwake.+

  • Salimo 18:kam
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • Kwa wotsogolera nyimbo. Salimo la mtumiki wa Yehova, Davide, amene anauza Yehova mawu a m’nyimbo iyi pa tsiku limene Yehova anamulanditsa m’manja mwa adani ake onse komanso m’manja mwa Sauli.+ Iye anati:

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena