Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Mapazi a okhulupirika ake amawateteza.+

      Koma anthu oipa amawawononga mu mdima,+

      Pakuti munthu sakhala wapamwamba chifukwa cha mphamvu zake.+

  • Salimo 33:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Taonani! Diso la Yehova lili pa anthu amene amamuopa,+

      Amene amayembekezera kukoma mtima kwake kosatha,+

  • Salimo 54:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Taonani! Mulungu ndiye mthandizi wanga.+

      Yehova ali pakati pa anthu amene akuchirikiza moyo wanga.

  • Salimo 124:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Moyo wathu uli ngati mbalame imene yathawa+

      Pamsampha wa munthu wogwiritsa ntchito nyambo.+

      Msamphawo wathyoka,+

      Ndipo ife tapulumuka.+

  • Miyambo 21:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Palibe nzeru kapena kuzindikira kulikonse, kapena malangizo alionse otsutsana ndi Yehova.+

  • Aroma 8:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena