Salimo 37:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Woipa amalondalonda munthu wolungama,+Ndipo amafuna kuti amuphe.+ Luka 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma iye anangodutsa pakati pawo n’kumapita.+ Yohane 8:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Pamenepo anatola miyala kuti amugende nayo,+ koma Yesu anabisala ndi kutuluka m’kachisimo.