Yohane 10:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Apanso Ayudawo anatola miyala kuti amugende.+ Yohane 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ophunzirawo anati: “Rabi,+ posachedwapa Ayudeya anafuna kukuponyani miyala,+ ndiye mukufuna kupitanso komweko kodi?”
8 Ophunzirawo anati: “Rabi,+ posachedwapa Ayudeya anafuna kukuponyani miyala,+ ndiye mukufuna kupitanso komweko kodi?”