Yohane 8:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Pamenepo anatola miyala kuti amugende nayo,+ koma Yesu anabisala ndi kutuluka m’kachisimo. Yohane 10:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Apanso Ayudawo anatola miyala kuti amugende.+