1 Samueli 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zitatero, Sauli anafuna kulasa Davide kuti amukhomerere kukhoma ndi mkondo.+ Koma Davide anaulewa+ pamaso pa Sauli, moti mkondowo unalasa khoma. Pamenepo, Davide anathawa kuti adzipulumutse usiku umenewo.+ 1 Samueli 20:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Atatero, Sauli anaponya mkondo wake kuti amulase.+ Pamenepo Yonatani anadziwa kuti bambo ake anatsimikiza mtima kupha Davide.+
10 Zitatero, Sauli anafuna kulasa Davide kuti amukhomerere kukhoma ndi mkondo.+ Koma Davide anaulewa+ pamaso pa Sauli, moti mkondowo unalasa khoma. Pamenepo, Davide anathawa kuti adzipulumutse usiku umenewo.+
33 Atatero, Sauli anaponya mkondo wake kuti amulase.+ Pamenepo Yonatani anadziwa kuti bambo ake anatsimikiza mtima kupha Davide.+