1 Samueli 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngati anganene kuti, ‘Palibe vuto!’ ndiye kuti zinthu zili bwino kwa mtumiki wako. Koma ngati angakwiye, udziwe kuti atsimikiza mtima kuchita kenakake koipa.+
7 Ngati anganene kuti, ‘Palibe vuto!’ ndiye kuti zinthu zili bwino kwa mtumiki wako. Koma ngati angakwiye, udziwe kuti atsimikiza mtima kuchita kenakake koipa.+