Miyambo 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mkwiyo umasefukira ndipo ukali ndi wankhanza,+ koma nsanje ndani angaipirire?+ 1 Yohane 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Aliyense amene amadana+ ndi m’bale wake ndi wopha munthu,+ ndipo mukudziwa kuti aliyense wopha munthu+ sadzalandira moyo wosatha.+ 1 Yohane 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ngati wina amanena kuti: “Ndimakonda Mulungu,” koma amadana ndi m’bale wake, ndiye kuti ndi wabodza.+ Pakuti amene sakonda m’bale wake+ amene amamuona, sangakonde Mulungu amene sanamuonepo.+
15 Aliyense amene amadana+ ndi m’bale wake ndi wopha munthu,+ ndipo mukudziwa kuti aliyense wopha munthu+ sadzalandira moyo wosatha.+
20 Ngati wina amanena kuti: “Ndimakonda Mulungu,” koma amadana ndi m’bale wake, ndiye kuti ndi wabodza.+ Pakuti amene sakonda m’bale wake+ amene amamuona, sangakonde Mulungu amene sanamuonepo.+