1 Yohane 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Okondedwa, tsopano ndife ana a Mulungu,+ koma padakali pano sizinaonekerebe kuti tidzakhala otani.+ Tikudziwa kuti akadzaonekera,+ tidzakhala ngati iyeyo,+ chifukwa tidzamuona mmene alili.+ 1 Yohane 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Palibe amene anaonapo Mulungu.+ Tikapitiriza kukondana, Mulungu apitiriza kukhala mwa ife ndipo chikondi chake kwa ife chikhala chokwanira.+
2 Okondedwa, tsopano ndife ana a Mulungu,+ koma padakali pano sizinaonekerebe kuti tidzakhala otani.+ Tikudziwa kuti akadzaonekera,+ tidzakhala ngati iyeyo,+ chifukwa tidzamuona mmene alili.+
12 Palibe amene anaonapo Mulungu.+ Tikapitiriza kukondana, Mulungu apitiriza kukhala mwa ife ndipo chikondi chake kwa ife chikhala chokwanira.+