-
2 Petulo 1:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Kudzera mwa zimenezi, iye watilonjeza zinthu zamtengo wapatali ndi zazikulu kwambiri,+ kuti mwa malonjezo amenewa mukhale ndi makhalidwe+ a Mulungu.+ Iye watipatsa kwaulere malonjezo amenewa chifukwa tapulumuka ku khalidwe loipa limene lili m’dzikoli,+ limene limayamba chifukwa cha chilakolako choipa.
-