Yohane 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiponso, ndikapita kukakukonzerani malo, ndidzabweranso+ kudzakutengerani kwathu,+ kuti kumene kuli ineko inunso mukakhale kumeneko.+ Aheberi 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 pamsonkhano wawo waukulu.+ Kumenenso kuli mpingo wa woyamba kubadwayo,+ mpingo wa iwo amene analembedwa+ kumwamba. Kumeneko kulinso Mulungu, Woweruza wa onse,+ ndiponso kuli moyo wauzimu wa olungama+ amene akhala angwiro.+
3 Ndiponso, ndikapita kukakukonzerani malo, ndidzabweranso+ kudzakutengerani kwathu,+ kuti kumene kuli ineko inunso mukakhale kumeneko.+
23 pamsonkhano wawo waukulu.+ Kumenenso kuli mpingo wa woyamba kubadwayo,+ mpingo wa iwo amene analembedwa+ kumwamba. Kumeneko kulinso Mulungu, Woweruza wa onse,+ ndiponso kuli moyo wauzimu wa olungama+ amene akhala angwiro.+