23 Ndapanikizika ndi zinthu ziwirizi,+ koma chimene ndikufuna ndicho kumasuka ndi kukhala ndi Khristu.+ Pakuti kunena zoona, chimenechi ndiye chabwino kwambiri.+
16 Chifukwa Ambuye mwini adzatsika kumwamba,+ ndi mfuu yolamula ya mawu a mkulu wa angelo,+ ndi lipenga+ la Mulungu. Ndipo amene anafa mwa Khristu adzauka choyamba.+