Luka 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 kuti mukadye+ ndi kumwa patebulo langa mu ufumu wanga,+ ndipo mukakhala m’mipando yachifumu+ kuweruza mafuko 12 a Isiraeli. Yohane 12:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ngati munthu wafuna kunditumikira ine, anditsatire, ndipo kumene ine ndidzakhala, mtumiki wanga adzakhalanso komweko.+ Aliyense wonditumikira ine, Atate adzamulemekeza.+ 1 Atesalonika 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pambuyo pake ife amoyo otsalafe, limodzi ndi iwowo,+ tidzatengedwa+ m’mitambo+ kukakumana+ ndi Ambuye m’mlengalenga, ndipo tizikakhala ndi Ambuye nthawi zonse.+
30 kuti mukadye+ ndi kumwa patebulo langa mu ufumu wanga,+ ndipo mukakhala m’mipando yachifumu+ kuweruza mafuko 12 a Isiraeli.
26 Ngati munthu wafuna kunditumikira ine, anditsatire, ndipo kumene ine ndidzakhala, mtumiki wanga adzakhalanso komweko.+ Aliyense wonditumikira ine, Atate adzamulemekeza.+
17 Pambuyo pake ife amoyo otsalafe, limodzi ndi iwowo,+ tidzatengedwa+ m’mitambo+ kukakumana+ ndi Ambuye m’mlengalenga, ndipo tizikakhala ndi Ambuye nthawi zonse.+