Machitidwe 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atatsiriza kunena zimenezi, Mulungu anamunyamula kupita m’mlengalenga iwo akuonerera,+ ndipo mtambo unamuphimba moti sanathenso kumuona.+ 2 Akorinto 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma tikulimba mtima ndipo ndife okondwa kukakhala ndi Ambuye, m’malo mokhala m’thupi linoli.+ Afilipi 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndapanikizika ndi zinthu ziwirizi,+ koma chimene ndikufuna ndicho kumasuka ndi kukhala ndi Khristu.+ Pakuti kunena zoona, chimenechi ndiye chabwino kwambiri.+
9 Atatsiriza kunena zimenezi, Mulungu anamunyamula kupita m’mlengalenga iwo akuonerera,+ ndipo mtambo unamuphimba moti sanathenso kumuona.+
23 Ndapanikizika ndi zinthu ziwirizi,+ koma chimene ndikufuna ndicho kumasuka ndi kukhala ndi Khristu.+ Pakuti kunena zoona, chimenechi ndiye chabwino kwambiri.+