Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 19:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Yesu anawayankha kuti: “Ndithu ndikukuuzani, Pa nthawi ya kulenganso zinthu, pamene Mwana wa munthu adzakhala pampando wachifumu waulemerero, inu amene mwatsatira ine mudzakhalanso m’mipando yachifumu 12, kuweruza mafuko 12 a Isiraeli.+

  • 1 Akorinto 6:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kapena simukudziwa kuti oyerawo adzaweruza+ dziko?+ Ndipo ngati mudzaweruza dziko, kodi simungathe kuzenga milandu yaing’ono kwambiri+ ngati imeneyo?

  • Chivumbulutso 2:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ndipo amene wapambana pa nkhondo ndi kutsatira zochita zanga kufikira mapeto,+ ndidzamupatsa ulamuliro pa mitundu ya anthu.+

  • Chivumbulutso 3:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Wopambana pa nkhondo+ ndidzamulola kukhala nane pampando wanga wachifumu,+ monga mmene ine ndinakhalira+ ndi Atate wanga pampando wawo wachifumu+ nditapambana pa nkhondo.

  • Chivumbulutso 20:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Wodala+ ndi woyera+ ndiye aliyense wouka nawo pa kuuka koyamba. Pa iwo, imfa yachiwiri+ ilibe ulamuliro.+ Koma adzakhala ansembe+ a Mulungu ndi a Khristu, ndipo adzalamulira monga mafumu limodzi naye zaka 1,000.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena