Chivumbulutso 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amene wapambana pankhondo+ ndidzamulola kuti akhale ndi ine pampando wanga wachifumu,+ ngati mmene ine ndinakhalira+ ndi Atate wanga pampando wawo wachifumu nditapambana pankhondo. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:21 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 72-73 Nsanja ya Olonda,5/15/2003, tsa. 20
21 Amene wapambana pankhondo+ ndidzamulola kuti akhale ndi ine pampando wanga wachifumu,+ ngati mmene ine ndinakhalira+ ndi Atate wanga pampando wawo wachifumu nditapambana pankhondo.