Yohane 12:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ngati munthu wafuna kunditumikira ine, anditsatire, ndipo kumene ine ndidzakhala, mtumiki wanga adzakhalanso komweko.+ Aliyense wonditumikira ine, Atate adzamulemekeza.+ Yohane 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atate, ine ndikufuna kuti amene mwandipatsawa adzakhale limodzi ndi ine kumene ine ndidzakhale,+ kuti adzaone ulemerero wanga umene inu mwandipatsa, chifukwa munandikonda musanayale maziko+ a dziko.+ 2 Atesalonika 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komabe abale, za kukhalapo*+ kwa Ambuye wathu Yesu Khristu, ndi kusonkhanitsidwa kwathu kwa iye,+ tikukupemphani
26 Ngati munthu wafuna kunditumikira ine, anditsatire, ndipo kumene ine ndidzakhala, mtumiki wanga adzakhalanso komweko.+ Aliyense wonditumikira ine, Atate adzamulemekeza.+
24 Atate, ine ndikufuna kuti amene mwandipatsawa adzakhale limodzi ndi ine kumene ine ndidzakhale,+ kuti adzaone ulemerero wanga umene inu mwandipatsa, chifukwa munandikonda musanayale maziko+ a dziko.+
2 Komabe abale, za kukhalapo*+ kwa Ambuye wathu Yesu Khristu, ndi kusonkhanitsidwa kwathu kwa iye,+ tikukupemphani