Luka 12:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Odala ndi akapolo amene mbuye wawo pofika adzawapeza akudikira!+ Ndithu ndikukuuzani, Iye adzamanga m’chiuno+ mwake ndi kuwakhazika patebulo kuti adye chakudya ndipo adzawatumikira.+ Chivumbulutso 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mngeloyo anandiuza kuti: “Lemba: Odala ndiwo amene aitanidwa+ ku phwando la chakudya chamadzulo la ukwati+ wa Mwanawankhosa.” Anandiuzanso kuti: “Awa ndi mawu oona a Mulungu.”+
37 Odala ndi akapolo amene mbuye wawo pofika adzawapeza akudikira!+ Ndithu ndikukuuzani, Iye adzamanga m’chiuno+ mwake ndi kuwakhazika patebulo kuti adye chakudya ndipo adzawatumikira.+
9 Mngeloyo anandiuza kuti: “Lemba: Odala ndiwo amene aitanidwa+ ku phwando la chakudya chamadzulo la ukwati+ wa Mwanawankhosa.” Anandiuzanso kuti: “Awa ndi mawu oona a Mulungu.”+