Mateyu 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Odala ndi anthu oyera mtima,+ chifukwa adzaona Mulungu.+ Yohane 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mulungu ndiye Mzimu,+ ndipo onse omulambira ayenera kumulambira motsogoleredwa ndi mzimu ndi choonadi.”+
24 Mulungu ndiye Mzimu,+ ndipo onse omulambira ayenera kumulambira motsogoleredwa ndi mzimu ndi choonadi.”+