1 Yohane 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Palibe amene anaonapo Mulungu.+ Tikapitiriza kukondana, Mulungu apitiriza kukhala nafe ndipo azitisonyeza chikondi chake mokwanira.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:12 Nsanja ya Olonda,2/1/1987, tsa. 15
12 Palibe amene anaonapo Mulungu.+ Tikapitiriza kukondana, Mulungu apitiriza kukhala nafe ndipo azitisonyeza chikondi chake mokwanira.+