-
Ekisodo 33:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ndiyeno anawonjezera kuti: “Sungathe kuona nkhope yanga, chifukwa palibe munthu amene angandione nʼkukhalabe ndi moyo.”
-