1 Samueli 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komanso, n’zosatheka kuti ineyo ndichimwire Yehova mwa kusiya kukupemphererani.+ Ndipo ndiyenera kukulangizani+ za njira yabwino+ ndi yolondola. Mateyu 5:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Koma ine ndikukuuzani kuti: Pitirizani kukonda adani anu+ ndi kupempherera amene akukuzunzani,+
23 Komanso, n’zosatheka kuti ineyo ndichimwire Yehova mwa kusiya kukupemphererani.+ Ndipo ndiyenera kukulangizani+ za njira yabwino+ ndi yolondola.