Aroma 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mulungu, amene ndikumuchitira utumiki wopatulika ndi moyo wanga wonse polalikira uthenga wabwino wonena za Mwana wake, ndiye mboni yanga+ ya mmene ndimakutchulirani m’mapemphero anga nthawi zonse.+ Akolose 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 N’chifukwa chake ifenso, kuyambira tsiku limene tinamva zimenezo, sitinaleke kukupemphererani.+ Takhala tikupemphanso kuti mukhale odziwa molondola+ chifuniro chake, ndiponso kuti mukhale ndi nzeru+ zonse komanso muzimvetsetsa zinthu zauzimu.+ 2 Timoteyo 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndikuyamika Mulungu, amene ndikumuchitira utumiki wopatulika+ monga mmene makolo anga+ anachitira, ndipo ndikuuchita ndi chikumbumtima choyera.+ Ndikumuyamika chifukwa chakuti sindiiwala za iwe m’mapembedzero anga,+ usana ndi usiku,
9 Mulungu, amene ndikumuchitira utumiki wopatulika ndi moyo wanga wonse polalikira uthenga wabwino wonena za Mwana wake, ndiye mboni yanga+ ya mmene ndimakutchulirani m’mapemphero anga nthawi zonse.+
9 N’chifukwa chake ifenso, kuyambira tsiku limene tinamva zimenezo, sitinaleke kukupemphererani.+ Takhala tikupemphanso kuti mukhale odziwa molondola+ chifuniro chake, ndiponso kuti mukhale ndi nzeru+ zonse komanso muzimvetsetsa zinthu zauzimu.+
3 Ndikuyamika Mulungu, amene ndikumuchitira utumiki wopatulika+ monga mmene makolo anga+ anachitira, ndipo ndikuuchita ndi chikumbumtima choyera.+ Ndikumuyamika chifukwa chakuti sindiiwala za iwe m’mapembedzero anga,+ usana ndi usiku,