Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Luka 6:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Pitirizani kudalitsa okutembererani ndi kupempherera amene akukunyozani.+

  • Luka 23:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 [[Koma Yesu anati: “Atate, akhululukireni,+ chifukwa sakudziwa chimene akuchita.”]]* Ndipo iwo anagawana malaya ake mwa kuchita maere.+

  • Machitidwe 7:60
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 60 Kenako anagwada pansi ndi kufuula ndi mawu amphamvu kuti: “Yehova, musawaimbe mlandu wa tchimo ili.”+ Atanena zimenezi anagona tulo ta imfa.

  • Aroma 12:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pitirizani kudalitsa anthu amene amakuzunzani.+ Muzidalitsa,+ osatemberera ayi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena