Machitidwe 11:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ndipo atamupeza anabwera naye ku Antiokeya. Choncho iwo anasonkhana ndi mpingo kumeneko chaka chonse, ndipo anaphunzitsa anthu ambirimbiri. Ku Antiokeya, n’kumene ophunzirawo anayamba kutchedwa Akhristu, motsogoleredwa ndi Mulungu.+ Machitidwe 15:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Koma Paulo ndi Baranaba anatsalira ku Antiokeya.+ Ndipo iwo pamodzi ndi enanso ambiri anali kuphunzitsa ndi kulengeza uthenga wabwino wa mawu a Yehova.+
26 ndipo atamupeza anabwera naye ku Antiokeya. Choncho iwo anasonkhana ndi mpingo kumeneko chaka chonse, ndipo anaphunzitsa anthu ambirimbiri. Ku Antiokeya, n’kumene ophunzirawo anayamba kutchedwa Akhristu, motsogoleredwa ndi Mulungu.+
35 Koma Paulo ndi Baranaba anatsalira ku Antiokeya.+ Ndipo iwo pamodzi ndi enanso ambiri anali kuphunzitsa ndi kulengeza uthenga wabwino wa mawu a Yehova.+