2 Samueli 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Natani anauza Davide kuti: “Munthu ameneyo ndiwe! Choncho Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ine ndinakudzoza+ iwe kuti ukhale mfumu ya Isiraeli ndipo ndinakupulumutsa+ m’manja mwa Sauli. Salimo 141:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza kukoma mtima kosatha,+Ndipo akandidzudzula ndiye kuti wandidzoza mafuta pamutu panga,+Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+Pakuti ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera.+ Chivumbulutso 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Onse amene ndimawakonda, ndimawadzudzula ndi kuwalanga.+ Choncho, khala wodzipereka ndipo ulape.+
7 Pamenepo Natani anauza Davide kuti: “Munthu ameneyo ndiwe! Choncho Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ine ndinakudzoza+ iwe kuti ukhale mfumu ya Isiraeli ndipo ndinakupulumutsa+ m’manja mwa Sauli.
5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza kukoma mtima kosatha,+Ndipo akandidzudzula ndiye kuti wandidzoza mafuta pamutu panga,+Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+Pakuti ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera.+
19 “‘Onse amene ndimawakonda, ndimawadzudzula ndi kuwalanga.+ Choncho, khala wodzipereka ndipo ulape.+