Salimo 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mumandipatsa chakudya patebulo, pamaso pa anthu ondichitira zoipa.+Mwadzoza mutu wanga ndi mafuta.+Chikho changa ndi chodzaza bwino.+ Miyambo 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti lamulolo ndilo nyale,+ ndipo malangizo ndiwo kuwala,+ komanso kudzudzula* kowongola zolakwa ndiko njira yamoyo,+ Miyambo 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Menya wonyoza+ kuti wosadziwa zinthu achenjere.+ Ndipo womvetsa zinthu uyenera kum’dzudzula kuti adziwe zinthu zowonjezereka.+ Yakobo 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi pali wina amene akudwala pakati panu?+ Aitane akulu a mpingo,+ ndipo iwo amupempherere ndi kumupaka mafuta+ m’dzina la Yehova.
5 Mumandipatsa chakudya patebulo, pamaso pa anthu ondichitira zoipa.+Mwadzoza mutu wanga ndi mafuta.+Chikho changa ndi chodzaza bwino.+
23 Pakuti lamulolo ndilo nyale,+ ndipo malangizo ndiwo kuwala,+ komanso kudzudzula* kowongola zolakwa ndiko njira yamoyo,+
25 Menya wonyoza+ kuti wosadziwa zinthu achenjere.+ Ndipo womvetsa zinthu uyenera kum’dzudzula kuti adziwe zinthu zowonjezereka.+
14 Kodi pali wina amene akudwala pakati panu?+ Aitane akulu a mpingo,+ ndipo iwo amupempherere ndi kumupaka mafuta+ m’dzina la Yehova.