Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Umuuze kuti ndidzaweruza nyumba yake+ mpaka kalekale chifukwa cha cholakwa ichi: Iye akudziwa+ kuti ana ake akunyoza Mulungu+ koma sakuwadzudzula.+

  • Miyambo 13:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Munthu wosakwapula mwana wake ndiye kuti akumuda,+ koma womukonda ndi amene amamuyang’anira kuti amulangize.+

  • Miyambo 22:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Phunzitsa mwana m’njira yomuyenerera.+ Ngakhale akadzakalamba sadzapatukamo.+

  • Miyambo 22:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Uchitsiru umakhazikika mumtima mwa mwana.+ Koma ndodo yomulangira* ndi imene imauthamangitsira kutali ndi iye.+

  • Miyambo 23:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Usam’mane chilango* mwana.+ Ngakhale utam’kwapula ndi chikwapu, sangafe ayi.

  • Miyambo 29:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Chikwapu ndi chidzudzulo n’zimene zimapereka nzeru,+ koma mwana womulekerera adzachititsa manyazi mayi ake.+

  • Aheberi 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kupirira kumene mukupiriraku,+ mukupirira kuti chikhale chilango chanu. Mulungu akuchita nanu zinthu ngati ana ake.+ Ndi mwana wanji amene bambo ake samulanga?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena