Miyambo 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu wosakwapula mwana wake ndiye kuti akumuda,+ koma womukonda ndi amene amamuyang’anira kuti amulangize.+ Miyambo 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Langa mwana wako padakali chiyembekezo,+ ndipo usalakelake imfa yake.+ Miyambo 29:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chikwapu ndi chidzudzulo n’zimene zimapereka nzeru,+ koma mwana womulekerera adzachititsa manyazi mayi ake.+ Miyambo 29:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Langa mwana wako ndipo adzakupatsa mpumulo ndiponso adzasangalatsa kwambiri moyo wako.+ Aefeso 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inunso abambo, musamapsetse mtima ana anu,+ koma muwalere+ m’malangizo*+ a Yehova* ndi kuwaphunzitsa kaganizidwe+ kake.
24 Munthu wosakwapula mwana wake ndiye kuti akumuda,+ koma womukonda ndi amene amamuyang’anira kuti amulangize.+
15 Chikwapu ndi chidzudzulo n’zimene zimapereka nzeru,+ koma mwana womulekerera adzachititsa manyazi mayi ake.+
4 Inunso abambo, musamapsetse mtima ana anu,+ koma muwalere+ m’malangizo*+ a Yehova* ndi kuwaphunzitsa kaganizidwe+ kake.