Miyambo 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu wosakwapula mwana wake ndiye kuti akumuda,+ koma womukonda ndi amene amamuyang’anira kuti amulangize.+ Miyambo 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Langa mwana wako padakali chiyembekezo,+ ndipo usalakelake imfa yake.+ Aheberi 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zoonadi, palibe chilango chimene chimamveka chosangalatsa pa nthawi yomwe ukuchilandira, koma chimakhala chowawa.+ Komabe pambuyo pake, kwa anthu amene aphunzirapo kanthu pa chilangocho, chimabala chipatso chamtendere,+ chomwe ndi chilungamo.+
24 Munthu wosakwapula mwana wake ndiye kuti akumuda,+ koma womukonda ndi amene amamuyang’anira kuti amulangize.+
11 Zoonadi, palibe chilango chimene chimamveka chosangalatsa pa nthawi yomwe ukuchilandira, koma chimakhala chowawa.+ Komabe pambuyo pake, kwa anthu amene aphunzirapo kanthu pa chilangocho, chimabala chipatso chamtendere,+ chomwe ndi chilungamo.+