Afilipi 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Muchite zimenezi kutinso mudzazidwe ndi zipatso zolungama+ kudzera mwa Yesu Khristu, kuti Mulungu akalemekezedwe ndi kutamandidwa.+ Yakobo 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Komanso, chilungamo+ ndicho chipatso+ cha mbewu zimene anthu odzetsa mtendere+ amafesa mu mtendere.+
11 Muchite zimenezi kutinso mudzazidwe ndi zipatso zolungama+ kudzera mwa Yesu Khristu, kuti Mulungu akalemekezedwe ndi kutamandidwa.+
18 Komanso, chilungamo+ ndicho chipatso+ cha mbewu zimene anthu odzetsa mtendere+ amafesa mu mtendere.+