Aefeso 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 umene ndi chikole+ cha cholowa chathu cham’tsogolo,+ kuti anthu a Mulungu+ adzamasulidwe ndi dipo,+ n’cholinga choti iye adzatamandidwe ndi kupatsidwa ulemerero.
14 umene ndi chikole+ cha cholowa chathu cham’tsogolo,+ kuti anthu a Mulungu+ adzamasulidwe ndi dipo,+ n’cholinga choti iye adzatamandidwe ndi kupatsidwa ulemerero.