Yohane 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndine mtengo wa mpesa, inu ndinu nthambi zake. Amene ali wolumikizika kwa ine, inenso n’kukhala wolumikizika kwa iye, ameneyo amabala zipatso zochuluka,+ chifukwa simungathe kuchita kalikonse popanda ine. Yakobo 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Komanso, chilungamo+ ndicho chipatso+ cha mbewu zimene anthu odzetsa mtendere+ amafesa mu mtendere.+
5 Ine ndine mtengo wa mpesa, inu ndinu nthambi zake. Amene ali wolumikizika kwa ine, inenso n’kukhala wolumikizika kwa iye, ameneyo amabala zipatso zochuluka,+ chifukwa simungathe kuchita kalikonse popanda ine.
18 Komanso, chilungamo+ ndicho chipatso+ cha mbewu zimene anthu odzetsa mtendere+ amafesa mu mtendere.+