Yohane 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndine mtengo wa mpesa, inu ndinu nthambi zake. Aliyense amene ali wolumikizika kwa ine, inenso nʼkukhala wolumikizika kwa iye, amabereka zipatso zochuluka+ chifukwa simungathe kuchita chilichonse popanda ine. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:5 Yesu—Ndi Njira, tsa. 276 Nsanja ya Olonda,8/15/1990, tsa. 8
5 Ine ndine mtengo wa mpesa, inu ndinu nthambi zake. Aliyense amene ali wolumikizika kwa ine, inenso nʼkukhala wolumikizika kwa iye, amabereka zipatso zochuluka+ chifukwa simungathe kuchita chilichonse popanda ine.