Miyambo 11:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zipatso za munthu wolungama ndizo mtengo wa moyo,+ ndipo munthu wopulumutsa miyoyo ndi wanzeru.+ Hoseya 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Efuraimu adzanena kuti, ‘Kodi mafano ndi a chiyaninso kwa ine?’+ “Ine ndidzamva ndipo ndidzapitirizabe kumuyang’anira.+ Ine ndili ngati mtengo waukulu wa mkungudza wamasamba obiriwira+ ndipo mudzapeza zipatso kwa ine.” Yohane 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Inu simunandisankhe ine, koma ine ndinakusankhani. Ndinakuikani kuti mupitirize kubala zipatso zochuluka,+ ndi kutinso zipatso zanuzo zisathe, kuti chilichonse chimene mungapemphe Atate m’dzina langa akupatseni.+ Agalatiya 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma makhalidwe* amene mzimu woyera umatulutsa+ ndiwo chikondi, chimwemwe, mtendere, kuleza mtima, kukoma mtima, ubwino,+ chikhulupiriro,
8 “Efuraimu adzanena kuti, ‘Kodi mafano ndi a chiyaninso kwa ine?’+ “Ine ndidzamva ndipo ndidzapitirizabe kumuyang’anira.+ Ine ndili ngati mtengo waukulu wa mkungudza wamasamba obiriwira+ ndipo mudzapeza zipatso kwa ine.”
16 Inu simunandisankhe ine, koma ine ndinakusankhani. Ndinakuikani kuti mupitirize kubala zipatso zochuluka,+ ndi kutinso zipatso zanuzo zisathe, kuti chilichonse chimene mungapemphe Atate m’dzina langa akupatseni.+
22 Koma makhalidwe* amene mzimu woyera umatulutsa+ ndiwo chikondi, chimwemwe, mtendere, kuleza mtima, kukoma mtima, ubwino,+ chikhulupiriro,