Hoseya 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Dziko la Asuri silidzatipulumutsa.+ Ife sitidzakwera pamahatchi.+ Sitidzauzanso ntchito ya manja athu kuti: “Inu Mulungu wathu!” chifukwa inu mumachitira chifundo mwana wamasiye.’*+ Machitidwe 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu ambiri amene anakhala okhulupirira anali kubwera kudzaulula machimo+ awo ndi kufotokoza poyera zoipa zimene anali kuchita.
3 Dziko la Asuri silidzatipulumutsa.+ Ife sitidzakwera pamahatchi.+ Sitidzauzanso ntchito ya manja athu kuti: “Inu Mulungu wathu!” chifukwa inu mumachitira chifundo mwana wamasiye.’*+
18 Anthu ambiri amene anakhala okhulupirira anali kubwera kudzaulula machimo+ awo ndi kufotokoza poyera zoipa zimene anali kuchita.