-
Machitidwe 19:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Anthu ambiri amene anakhala okhulupirira ankabwera kudzaulula machimo awo ndiponso kufotokoza poyera zoipa zimene ankachita.
-