Machitidwe 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu ambiri amene anakhala okhulupirira anali kubwera kudzaulula machimo+ awo ndi kufotokoza poyera zoipa zimene anali kuchita.
18 Anthu ambiri amene anakhala okhulupirira anali kubwera kudzaulula machimo+ awo ndi kufotokoza poyera zoipa zimene anali kuchita.