1 Samueli 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Umuuze kuti ndidzaweruza nyumba yake+ mpaka kalekale chifukwa cha cholakwa ichi: Iye akudziwa+ kuti ana ake akunyoza Mulungu+ koma sakuwadzudzula.+ 1 Mafumu 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Bambo ake sanafune kumukhumudwitsa pa nthawi ina iliyonse, choncho sanam’dzudzulepo kuti: “Wachitiranji zinthu m’njira imeneyi?”+ Iye analinso wooneka bwino kwambiri,+ ndipo mayi ake anam’bereka pambuyo pobereka Abisalomu. Miyambo 29:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chikwapu ndi chidzudzulo n’zimene zimapereka nzeru,+ koma mwana womulekerera adzachititsa manyazi mayi ake.+
13 Umuuze kuti ndidzaweruza nyumba yake+ mpaka kalekale chifukwa cha cholakwa ichi: Iye akudziwa+ kuti ana ake akunyoza Mulungu+ koma sakuwadzudzula.+
6 Bambo ake sanafune kumukhumudwitsa pa nthawi ina iliyonse, choncho sanam’dzudzulepo kuti: “Wachitiranji zinthu m’njira imeneyi?”+ Iye analinso wooneka bwino kwambiri,+ ndipo mayi ake anam’bereka pambuyo pobereka Abisalomu.
15 Chikwapu ndi chidzudzulo n’zimene zimapereka nzeru,+ koma mwana womulekerera adzachititsa manyazi mayi ake.+