Genesis 27:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Zitatha izi, Rabeka anali kuuza Isaki nthawi ndi nthawi kuti: “Ndafika ponyansidwa nawo moyo wanga chifukwa cha ana aakazi achihetiwa.+ Ngati Yakobo atenga mkazi kuno pakati pa ana achiheti ngati amenewa, ndi bwino ndingofa!”+ Miyambo 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Miyambi ya Solomo.+ Mwana wanzeru amakondweretsa bambo ake,+ koma mwana wopusa amamvetsa chisoni mayi ake.+ Miyambo 17:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mwana wopusa amakhumudwitsa bambo ake,+ ndipo amamvetsa chisoni mayi ake amene anam’bereka.+
46 Zitatha izi, Rabeka anali kuuza Isaki nthawi ndi nthawi kuti: “Ndafika ponyansidwa nawo moyo wanga chifukwa cha ana aakazi achihetiwa.+ Ngati Yakobo atenga mkazi kuno pakati pa ana achiheti ngati amenewa, ndi bwino ndingofa!”+
10 Miyambi ya Solomo.+ Mwana wanzeru amakondweretsa bambo ake,+ koma mwana wopusa amamvetsa chisoni mayi ake.+