Genesis 26:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Akaziwo anabweretsa chisoni kwa Isaki ndi Rabeka.+ Genesis 28:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo Esau anazindikira kuti, Isaki bambo ake, anali kuipidwa nawo ana aakazi a ku Kanani.+