Miyambo 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwana wanzeru ndi amene amakondweretsa bambo ake,+ koma wopusa amanyoza mayi ake.+ Miyambo 17:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Bambo wa mwana wopusa amamva chisoni,+ ndipo bambo wa mwana wopanda nzeru sasangalala.+ Miyambo 17:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mwana wopusa amakhumudwitsa bambo ake,+ ndipo amamvetsa chisoni mayi ake amene anam’bereka.+