1 Mafumu 1:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Komanso mfumu inati, ‘Adalitsike+ Yehova Mulungu wa Isiraeli, amene lero wapereka munthu woti akhale pampando wanga wachifumu, ine ndikuona ndi maso anga.’”+ Miyambo 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mwana wanga, mtima wako ukakhala wanzeru,+ ndithu mtima wanga udzasangalala.+ Miyambo 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwana wanga, khala wanzeru ndi kukondweretsa mtima wanga,+ kuti ndimuyankhe amene akunditonza.+
48 Komanso mfumu inati, ‘Adalitsike+ Yehova Mulungu wa Isiraeli, amene lero wapereka munthu woti akhale pampando wanga wachifumu, ine ndikuona ndi maso anga.’”+