Miyambo 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Miyambi ya Solomo.+ Mwana wanzeru amakondweretsa bambo ake,+ koma mwana wopusa amamvetsa chisoni mayi ake.+ Miyambo 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwana wanga, khala wanzeru ndi kukondweretsa mtima wanga,+ kuti ndimuyankhe amene akunditonza.+ 3 Yohane 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Palibe chimene chimandisangalatsa kwambiri kuposa kumva kuti ana anga akuyendabe m’choonadi.+
10 Miyambi ya Solomo.+ Mwana wanzeru amakondweretsa bambo ake,+ koma mwana wopusa amamvetsa chisoni mayi ake.+