1 Akorinto 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti ngakhale mutakhala ndi aphunzitsi+ 10,000 mwa Khristu, ndithudi mulibe abambo ambiri,+ pakuti mwa Khristu Yesu ndakhala bambo anu kudzera mwa uthenga wabwino.+ 2 Timoteyo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndikulembera iwe Timoteyo mwana wanga wokondedwa:+ Kukoma mtima kwakukulu, chifundo, ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate ndi kwa Khristu Yesu Ambuye wathu+ zikhale nawe. Tito 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndikulembera Tito, mwana wanga+ weniweni m’chikhulupiriro chimodzi chomwe tili nacho: Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere wa Mulungu Atate+ ndi Khristu Yesu Mpulumutsi wathu,+ zikhale nawe. Filimoni 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndikukupempha za mwana wanga+ Onesimo,+ amene ndakhala bambo+ wake pamene ndili m’ndende.
15 Pakuti ngakhale mutakhala ndi aphunzitsi+ 10,000 mwa Khristu, ndithudi mulibe abambo ambiri,+ pakuti mwa Khristu Yesu ndakhala bambo anu kudzera mwa uthenga wabwino.+
2 ndikulembera iwe Timoteyo mwana wanga wokondedwa:+ Kukoma mtima kwakukulu, chifundo, ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate ndi kwa Khristu Yesu Ambuye wathu+ zikhale nawe.
4 Ndikulembera Tito, mwana wanga+ weniweni m’chikhulupiriro chimodzi chomwe tili nacho: Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere wa Mulungu Atate+ ndi Khristu Yesu Mpulumutsi wathu,+ zikhale nawe.